18/08/2024
Tikhala ndi training yophunzitsa momwe tingapangire Ena mwa ma products omwe Chambe investments ikupanga pakantengo kozizila ,monga pine gel osasungunuka or angakhale Chaka
Kupanga car shampoo yemwe amasunga mtundu wa galimoto(osasuluka)
Surf wa pompo kupanga nkuchapila
Bathing soap , Dish wash, Dish paste,
Dashbord cleaner , sugar ndizina zambiri for registration Whatsapp on
0997109395/ 0881794709