Active Pest control, Disinfection, Sanitizing & Cleaning services

Active Pest control, Disinfection, Sanitizing & Cleaning services Professional and affordable pest control services
(1)

mphevu zikachulukisa ngati izi zimapezeka mundiwo, mafuta ophikira, mu ufa ndi malo ena omwe mumasungapo zakudya. Tiziwi...
14/11/2025

mphevu zikachulukisa ngati izi zimapezeka mundiwo, mafuta ophikira, mu ufa ndi malo ena omwe mumasungapo zakudya. Tiziwiseni lero zisanafike apa tizapopere...0996698608

Timathana ndi nsikizi mphevu chiswe utitili makoswe nankafumbwe njuchi udzudzu ndizina popopera mankhwara.+265 996 698 6...
27/08/2025

Timathana ndi nsikizi mphevu chiswe utitili makoswe nankafumbwe njuchi udzudzu ndizina popopera mankhwara.
+265 996 698 608

Nthawi yolira ndichiswe sopano yatha chifukwa tili ndimankhwara amphavu okuti tikathira panyumba yanu yomwe munamanga ka...
17/07/2025

Nthawi yolira ndichiswe sopano yatha chifukwa tili ndimankhwara amphavu okuti tikathira panyumba yanu yomwe munamanga kale kapena pamalo omwe palibepo nyumba chiswecho chimaferatu pompo ndipo timapereka guarantee ya 5 years tikakuthirirani mankhwara.
Tili ku Blantyre ndi Lilongwe 0996698608

Tiyeseni lero ndipo simuzakhumudwa

We are Specialising in Plumbing and Tilling job's New Installation and Renovations *Sewerage drain Laying *Burst Pipe*St...
17/07/2025

We are Specialising in Plumbing and Tilling job's
New Installation and Renovations
*Sewerage drain Laying
*Burst Pipe
*Storm Water Drainages
*Sewerage Blockage
*Sanitary Installation
*Bathroom Renovations
*Leaking Valves and Tapes
And MORE
JUST GET IN TOUCH WITH US 0996698608

Pay for one house and have the next one sprayed for Free.0996698608Promotion only for 6 daysBlantyre
01/07/2025

Pay for one house and have the next one sprayed for Free.
0996698608
Promotion only for 6 days
Blantyre

We do water proofing torch on end painting roofing deck management fix and supply for more information contact use on th...
18/06/2025

We do water proofing torch on end painting roofing deck management fix and supply for more information contact use on this numbers 0996698608/ 0886279916

Timathana ndichiswe chantundu uliwose chomwe chikukusawusani pochithira mankhwara okupha chiswecho Kaya ndichulu Kaya ch...
16/06/2025

Timathana ndichiswe chantundu uliwose chomwe chikukusawusani pochithira mankhwara okupha chiswecho Kaya ndichulu Kaya choyenda ndikhoma Kaya chokudya kapinga Kaya chilikudenga kudya ceiling matabwa mitengo chonsecho chimathana nacho ndipo chimatheratu chiswecho pompo...
0996698608

Kodi mukusawusika ndi Chiswe komanso Mileme? Timapopera mankhwara okupha tizilomboti pantengo ozizira....Timapoperaso ns...
21/02/2025

Kodi mukusawusika ndi Chiswe komanso Mileme? Timapopera mankhwara okupha tizilomboti pantengo ozizira....

Timapoperaso nsikizi mphevu utitili makoswe ntchetche udzudzu analimata nyelele nankafumbwe njuchi njoka anankalizi ndizina zambiri....
+265 886 279 916 +265 996 698 608

Have you tried other means and it never worked? Try us today for complete one time EXTERMINATION of all nuisance pests.C...
12/12/2024

Have you tried other means and it never worked? Try us today for complete one time EXTERMINATION of all nuisance pests.

Contact us +265 996 698 608
+265 886 279 916

We offer WATERPROOFING SERVICES!Trust us to take care of your project (s)We waterproof the following areas ;●Flat roofs ...
30/10/2024

We offer WATERPROOFING SERVICES!

Trust us to take care of your project (s)

We waterproof the following areas ;

●Flat roofs
● Underground structures like tanks, basements etc
● Wet areas - Bathroom and laundry areas
● Existing roofs with bituminous felt
● Hidden Roofs
● Concrete gutters etc

For a site assessment or any inquiries
Call or WhatsApp 📞 +265 996 698 608 +265 886 279 916

Ndife akatakwe pankhani yopopera ndikupha tizilombo munga nsikizi, mphevu, makoswe, udzudzu, utitili, chiswe, Mileme, ny...
22/10/2024

Ndife akatakwe pankhani yopopera ndikupha tizilombo munga nsikizi, mphevu, makoswe, udzudzu, utitili, chiswe, Mileme, nyelele, anankalizi, nankafumbwe, njuchi, njoka, analimata, ntchetche nditizilombo tina tosiyana siyana....
Blantyre and Lilongwe
+ 265 996 698 608 +265 886 279 916

Looking for a team that is keen on detail, committed towards highest attainable standards of service? Call us today to s...
22/10/2024

Looking for a team that is keen on detail, committed towards highest attainable standards of service?
Call us today to schedule your appointment.
+265 996 698 608 +265 886 279 916

Address

Kabula
Blantyre

Telephone

+265996698608

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Active Pest control, Disinfection, Sanitizing & Cleaning services posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share