25/01/2026
Timapopera ndikupheratu tizilombo tosowetsa mtendere m'nyumba, Ma Warehouse komanso Ma office kapena malo ena aliwonse a business yanu monga
✅️Nsikidzi
✅️Mphenvu
✅️Udzudzu
✅️Anankalizi
✅️Chiswe
✅️Njuchi
✅️Njoka
✅️Abuluzi ndi zina zambiri.
☑️Komanso tili ndi mankhwala abwino ophela makoswe
Tipezeni in Limbe (Zulekha Arcade, Shop No. 19) Komanso in Lilongwe (Opposite Bwaila, Simso Filling Station).
Call/WhatsApp: +265 884 108 104 | 0995 67 31 46