KANJO Cleaning & Landscapers

KANJO Cleaning & Landscapers Landscaping and Cleaning service's

Ma  Rovers grass azawalaso monga Inu mufunila osaiwala makoma anu azawala mene mukuonelamo fumbi lisakusowetseni mtender...
24/08/2026

Ma Rovers grass azawalaso monga Inu mufunila osaiwala makoma anu azawala mene mukuonelamo fumbi lisakusowetseni mtendere ayi nyumba zanu zioneke bwino plz ndi KANJO cleaning simuzakhumudwa ayi tiyeseni

Ma.  Tailos anu azawala ngati mene munagulira chonde musachedwe mabwana tiitaneni basi
24/08/2026

Ma. Tailos anu azawala ngati mene munagulira chonde musachedwe mabwana tiitaneni basi

24/08/2026

General cleaning manyumba mwanu zimatheka muzayamika tiitaneni pano kwayamba mphepo Yi ikuononga makoma anu asanyase ayi tizakweche basi

24/08/2026

Mutiyese ife basi simuzakhumudwa yabwela kuzakhala iyo zonse zikutheka

Tiyeseni basi simuzakhumudwa abale anga mwayesa ena kwathawi sizimayenda koma ife ayi muzayamika
24/08/2026

Tiyeseni basi simuzakhumudwa abale anga mwayesa ena kwathawi sizimayenda koma ife ayi muzayamika

Zikumatheka tiyeseni simuzakhumudwa ayi
08/07/2026

Zikumatheka tiyeseni simuzakhumudwa ayi

Zikatheka kutchetcha kumaoneka bwino ntchito. Anthu ake ndi ndiifeyo basi plz tipatsekoni ntchito mutiyese muone mene ma...
08/07/2026

Zikatheka kutchetcha kumaoneka bwino ntchito. Anthu ake ndi ndiifeyo basi plz tipatsekoni ntchito mutiyese muone mene manja amagwirira ntchito yokoma

Address

Mulanje
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when KANJO Cleaning & Landscapers posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share